Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 100:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Pfuulirani kwa Yehova, inu, dziko lonse lapansi.

2. Tumikirani Yehova ndi cikondwerero:Idzani pamaso pace ndi kumyimbira mokondwera,

3. Dziwani kuti Yehova ndiye Mulungu;Iyeyu anatilenga, ndipo ife ndife ace;Ndife anthu ace ndi nkhosa za pabusa pace.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 100