WODALA munthuyo wosayenda mu uphungu wa oipa,Kapena wosaimirira m'njira ya ocimwa,Kapena wosakhala pansi pa bwalo la onyoza.