Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Maliro 1:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kodi muyesa cimeneci cabe, nonsenu opita panjira?Penyani nimuone, kodi ciripo cisoni cina ngati cangaci amandimvetsa ine,Cimene Yehova wandisautsa naco tsiku la mkwiyo wace waukali?

Werengani mutu wathunthu Maliro 1

Onani Maliro 1:12 nkhani