Taonani, ndidzaipsa mbeu cifukwa ca inu, ndi kuwaza ciphwidza pankhope panu, ndico ciphwidza ca nsembe zanu, ndipo adzakucotsani pamodzi naco.