Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 9:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anaphanso ng'ombe, ndi nkhosa yamphongoyo, ndizo nsembe zoyamika za anthu; ndi ana a Aroni anapereka kwa iye mwaziwo, ndipo anauwaza pa guwa la nsembe pozungulira, ndi mafuta a ng'ombe;

Werengani mutu wathunthu Levitiko 9

Onani Levitiko 9:18 nkhani