Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 7:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kunena za nyama ya nsembe volemekeza ya nsembe zoyamika zace, aziidya tsiku lomwelo lakuipereka; asasiyeko kufikira m'mawa.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 7

Onani Levitiko 7:15 nkhani