Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 7:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pa zopereka zonsezi atengepo ndi kubwera nako kamtanda kamodzi, kuti kakhale ka nsembe yokweza ya kwa Yehova; kakhale ka wansembe wakuwaza mwazi wa nsembe zoyamika.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 7

Onani Levitiko 7:14 nkhani