Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 7:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

akabwera nayo kuti ikhale nsembe yolemekeza, azibwera nato, pamodzi ndinsembe yolemekeza, timitanda topanda cotupitsa tosanganiza ndi mafuta, ndi timitanda taphanthi topanda cotupitsa todzoza ndi mafuta, ndi timitanda tooca, ta ufa wosalala tosanganiza ndi mafuta.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 7

Onani Levitiko 7:12 nkhani