Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 6:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pamenepo padzali kuti popeza anacimwa, naparamula, azibweza zofunkha zimene analanda mwacifwamba, kapena cinthuci adaciona ndi kusautsa mnzace, kapena coikiza anamuikiza, kapena cinthu cotayika anacipeza;

Werengani mutu wathunthu Levitiko 6

Onani Levitiko 6:4 nkhani