Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 6:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma asadye nsembe yaucimo iri yonse, imene amadza nao mwazi wace ku cihema cokomanako kutetezera nao m'malo opatulika; aitenthe ndi moto.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 6

Onani Levitiko 6:30 nkhani