Ndipo azidya iyi wansembe amene aipereka cifukwa ca zoipa; aidyere m'malo opatulika, pa bwalo la cihema cokomanako.