Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 6:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Lankhula ndi Aroni ndi ana ace, ndi kuti, Cilamulo ca nsembe yaucimo ndi ici: Pamalo pophera nsembe yopsereza ndipo pophera nsembe yaucimo pamaso pa Yehova; ndiyo yopatulikitsa.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 6

Onani Levitiko 6:25 nkhani