Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 6:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Amuna onse a mwa ana a Aroni adyeko, ndilo lemba losatha la ku mibadwo yanu, ciwacokere ku nsembe zamoto za Yehova; ali yense wakuzikhudza izi adzakhala wapatolika.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 6

Onani Levitiko 6:18 nkhani