Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 6:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Asaciphike ndi cotupitsa, Ndacipereka cikhale gawo lao locokera pa nsembe zanga zamoto; ndico copatulikitsa, monga nsembe yaucimo, ndi monga nsembe yoparamula.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 6

Onani Levitiko 6:17 nkhani