Ndipo munthu akacimwa, nakacita dna ca zinthu ziti zonse aziletsa Yehova; angakhale analibe kudziwa, koma waparamula, azisenza mphulupulu yace.