Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 4:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nacotse mafuta ace onse, monga umo amacotsera mafuta pa nsembe yoyamika; ndipo wansembeyo awatenthe pa guwa la nsembe akhale pfungo lokoma la kwa Yehova; ndi wansembe amcitire comtetezera, ndipo adzakhululukidwa.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 4

Onani Levitiko 4:31 nkhani