Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 3:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo abwere nayo nsembe yamoto ya kwa Yehova; yotengako ku nsembe yoyamika; mafuta ace, mcira wamafuta wonse, ataucotsa kufupi ku pfupa lao msana; naicotse mafuta akukuta matumbo, ndi mafuta onse akukhala pamatumbo,

Werengani mutu wathunthu Levitiko 3

Onani Levitiko 3:9 nkhani