Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 26:45-46 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

45. Koma cifukwa ca iwo ndidzawakumbukila pangano la makolo ao, amene ndinawaturutsa m'dziko la Aigupto pamaso pa amitundu, kuti ndikhale Mulungu wao; Ine ndine Yehova.

46. Awa ndi malemba ndi maweruzo ndi malamulo amene Yehova anaika pakati pa iye ndi ana a Israyeli m'phiri la Sinai, ndi dzanja la Mose.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 26