Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 26:45 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma cifukwa ca iwo ndidzawakumbukila pangano la makolo ao, amene ndinawaturutsa m'dziko la Aigupto pamaso pa amitundu, kuti ndikhale Mulungu wao; Ine ndine Yehova.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 26

Onani Levitiko 26:45 nkhani