Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 26:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndinakuturutsani m'dziko la Aigupto, kuti musakhale akapolo ao; ndipo ndinatyola mitengo ya magoli anu, ndi kukuyendetsani coweramuka.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 26

Onani Levitiko 26:13 nkhani