Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 25:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo munthu akagula kwa Mlevi, nyumba yogulayo yokhala m'mudzi wace wace, ituruke m'caka coliza lipenga, popeza nyumba za m'midzi ya Alevi ndizo zao zao mwa ana a Israyeli.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 25

Onani Levitiko 25:33 nkhani