Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 23:39 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma tsiku lakhumi ndi cisanu la mwezi wacisanu ndi ciwiri, mutatuta zipatso za m'dziko, muzisunga madyerero a Yehova masiku asanu ndi awiri; tsiku loyamba mupumule, ndi tsiku lacisanu ndi citatu mupumule.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 23

Onani Levitiko 23:39 nkhani