Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 23:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mubwere nao pamodzi ndi mikate, ana a nkhosa asanu ndi awiri, opanda cirema a caka cimodzi, ndi ng'ombe yamphongo imodzi, ndi nkhosa zamphongo ziwiri; zikhale nsembe yopsereza ya Yehova, pamodzi ndi nsembe yao yaufa, ndi nsembe zao zothira, ndizo nsembe yamoto ya pfungo lokoma la Yehova.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 23

Onani Levitiko 23:18 nkhani