Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 20:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo nkhope yanga idzatsutsana naye munthuyo, ndi kumsadza kumcotsa pakati pa anthu a mtundu wace; popeza anapereka a mbeu zace kwa Moleke, kudetsa nako malo anga opatulika, ndi kuipsa dzina langa lopatulika.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 20

Onani Levitiko 20:3 nkhani