Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 2:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo copereka cako ciri conse ca nsembe yaufa uzicikoleretsa ndi mcere; usasowe mcere wa cipangano ca Mulungu wako pa nsembe yako yaufa; pa zopereka zako zonse uzipereka mcere.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 2

Onani Levitiko 2:13 nkhani