Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 17:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

osadza nayo ku khomo la cihema cokomanako, kuti aipereke copereka ca Yehova, ku bwalo la kacisi wa Yehova; azimuyesa munthuyu wocimwira mwazi, wakhetsa mwazi; ndipo amsadze munthuyo kumcotsa pakati pa anthu a mtundu wace;

Werengani mutu wathunthu Levitiko 17

Onani Levitiko 17:4 nkhani