Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 16:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Abvale maraya a m'kati a bafuta wopatulika, nakhale nazo zobvala za kumiyendo pathupi pace, nadzimangire m'cuuno ndi mpango wabafuta, nabvale nduwira yabafuta; izi ndi zobvala zopatulika; potero asambe thupi lace ndi madzi, ndi kubvala izi.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 16

Onani Levitiko 16:4 nkhani