Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 16:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo asambe thupi lace ndi madzi kumalo kopatulika, nabvale zobvala zace, naturuke, napereke nsembe yopsereza yace, ndi nsembe yopsereza ya anthu, nacite codzitetezera yekha ndi anthu.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 16

Onani Levitiko 16:24 nkhani