Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 16:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo aiphe mbuzi ya nsembe yaucimo, ndiyo yophera anthu, nalowe nao mwazi wace m'tseri mwa nsaru yocinga, nacite nao mwazi wace monga umo anacitira ndi mwazi wa ng'ombe, nauwaze pacotetezerapo ndi cakuno ca cotetezerapo;

Werengani mutu wathunthu Levitiko 16

Onani Levitiko 16:15 nkhani