Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 15:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsiku lacisanu ndi citatu atenge njiwa ziwiri, kapena maunda awiri, nafike pamaso pa Yehova pa khomo la cihema cokomanako, nazipereke kwa wansembe;

Werengani mutu wathunthu Levitiko 15

Onani Levitiko 15:14 nkhani