Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 14:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo wansembe apakeko mafuta okh a ria m'dzanja lace pa ndewerere ya khutu la ku dzanja lamanja la iye wakuti ayeretsedwe, ndi pa cala cacikuru ca dzanja lace lamanja, ndi pa cala cacikuru ca phazi lace la ku dzanja lamanja, pa mwazi wa nsembe yoparamula;

Werengani mutu wathunthu Levitiko 14

Onani Levitiko 14:17 nkhani