Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 13:55 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo wansembe aone nthenda ataitsuka, ndipo taonani, ngati nthendayi siinasandulika maonekedwe ace, yosakulanso nthenda, ndico codetsedwa; ucitenthe ndi moto; ndilo pfunka, kungakhale kuyera kwace kuli patsogolo kapena kumbuyo.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 13

Onani Levitiko 13:55 nkhani