Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 13:46 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Masiku onse nthenda ikali pa iye azikhala wodetsedwa; ali wodetsedwa, agone pa yekha pokhala pace pakhale kunja kwa cigono.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 13

Onani Levitiko 13:46 nkhani