Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 13:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo Yehova ananena ndi Mose ndi Aroni, nati,

2. Ngati munthu ali naco cotupa, kapena nkhanambo, kapena cikanga pa khungu la thupi lace, ndipo isandulika nthenda yakhate pa khungu la thupi lace, azifika kwa Aroni wansembe, kapena kwa mmodzi wa ana ace ansembe;

Werengani mutu wathunthu Levitiko 13