Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 13:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo wansembe aione nthenda pa khungu la thupi; ndipo ngati tsitsi la panthenda lasanduka la mbu, ndi nthenda ikaoneka yapitirira khungu la thupi lace, ndiyo nthenda yakhate; ndipo wansembe amuone, namuche wodetsedwa.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 13

Onani Levitiko 13:3 nkhani