Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 11:45 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti Ine ndine Yehova amene ndinakukwezani kukuturutsani m'dziko la Aigupto, ndikhale Mulungu wanu; cifukwa cace mukhale oyera, popeza ine ndine woyera.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 11

Onani Levitiko 11:45 nkhani