Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 11:44 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti Ine ndine Yehova Mulungu wanu; potero dzipatuleni, ndipo muzikhala oyera; pakuti Ine ndine woyera; ndipo musamadziipsa ndi cokwawa ciri conse cakukwawa pansi.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 11

Onani Levitiko 11:44 nkhani