Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 10:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ana a Aroni, Nadabu ndi Abihu anatenga yense mbale yace ya zofukiza, naikamo moto, naikapo cofukiza, nabwera nao pamaso pa Yehova moto wacilendo, umene sanawauza.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 10

Onani Levitiko 10:1 nkhani