Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Hoseya 9:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndinapeza Israyeli ngati mphesa m'cipululu, ndinaona makolo anu ngati cipatso coyamba ca mkuyu nyengo yace yoyamba; koma anadza kwa Baala Peori, nadzipatulira conyansaco, nasandulika onyansa, conga cija anacikonda.

Werengani mutu wathunthu Hoseya 9

Onani Hoseya 9:10 nkhani