Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Hoseya 7:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

M'mene ndiciritsa Israyeli, mphulupulu ya Efraimu ibvumbuluka, ndi zoipa za Samariya; pakuti acita bodza, ndipo mkhungu alowa m'nyumba, ndi gulu la mbala manca kubwalo.

Werengani mutu wathunthu Hoseya 7

Onani Hoseya 7:1 nkhani