Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Hoseya 6:9-11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

9. Ndipo monga magulu a mbala alalira munthu, momwemo msonkhano wa ansembe amapha pa njira ya ku Sekemu; indedi acita coipitsitsa.

10. M'nyumba ya Israyeli ndinaona cinthu coopsetsa; pamenepo pali citole ca Efraimu; Israyeli wadetsedwa.

11. Akuikidwiratunso nyengo yakukolola, Yuda iwe, pamene ndikabwezanso undende wa anthu anga.

Werengani mutu wathunthu Hoseya 6