Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Hoseya 5:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamene Efraimu anaona nthenda yace, ndi Yuda bala lace, Efraimu anamuka kwa Asuri, natumiza kwa mfumu Yarebu; koma iye sakhoza kukuciritsani, kapena kupoletsa bala lanu.

Werengani mutu wathunthu Hoseya 5

Onani Hoseya 5:13 nkhani