Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Hoseya 3:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anati kwa ine, Mukanso, konda mkazi wokondedwa ndi bwenzi lace, koma wakucita cigololo monga Yehova akonda ana a Israyeli, angakhale atembenukira ku milungu yina, nakonda ncinci za mphesa zouma.

Werengani mutu wathunthu Hoseya 3

Onani Hoseya 3:1 nkhani