Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Hoseya 1:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

MAU a Yehova amene anadza kwa Hoseya mwana wa Beeri masiku a Uziya, Yotamu, Ahazi, ndi Hezekiya, mafumu a Yuda, ndi masiku a Yerobiamu mwana wa Yoasi mfumu ya Israyeli.

Werengani mutu wathunthu Hoseya 1

Onani Hoseya 1:1 nkhani