Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Habakuku 3:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anaimirira, nandengulitsa dziko lapansi;Anapenya, nanjenjemeretsa amitundu;Ndi mapiri acikhalire anamwazika,Zitunda za kale lomwe zinawerama;Mayendedwe ace ndiwo a kale lomwe.

Werengani mutu wathunthu Habakuku 3

Onani Habakuku 3:6 nkhani