Cinkana mkuyu suphuka,Kungakhale kulibe zipatso kumpesa;Yalephera nchito ya azitona,Ndi m'minda m'mosapatsa cakudya;Ndi zoweta zacotsedwa kukhola,Palibenso ng'ombe m'makola mwao;