Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Habakuku 3:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndinamva, ndi m'mimba mwanga munabwadamuka,Milomo yanga inanthunthumira pamau,M'mafupa mwanga mudalowa cibvundi, ndipo ndinanjenjemera m'malo mwanga;Kuti ndipumule tsiku lamsauko,Pamene akwerera anthu kuti ayambane nao ndi makamu.

Werengani mutu wathunthu Habakuku 3

Onani Habakuku 3:16 nkhani