Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Habakuku 2:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kodi sadzamnenera fanizo onsewo, ndi mwambi womnyodola, ndi kuti, Tsoka iye wocurukitsa zimene siziri zace! mpaka liti? iye wodzisenzera zigwiriro.

Werengani mutu wathunthu Habakuku 2

Onani Habakuku 2:6 nkhani