Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Habakuku 2:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ciwawa cidacitikira Lebano cidzakukuta, ndi cionongeko ca nyama cidzakuopsa; cifukwa ca mwazi wa anthu, ndi ciwawa cocitidwira dziko, mudzi, ndi onseokhalamo.

Werengani mutu wathunthu Habakuku 2

Onani Habakuku 2:17 nkhani