Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 9:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Amene akhetsa mwazi wa munthu, ndi munthunso mwazi wace udzakhetsedwa: cifukwa m'cifanizo ca Mulungu Iye anampanga munthu.

Werengani mutu wathunthu Genesis 9

Onani Genesis 9:6 nkhani